Allah Ta’alaa instructs us to be just in the Quraan Shareef. O believers! Stand firm …
Read More »Zowona pa Mahatchi (Chichewa)
Allah Ta’ala akunena kuti: “Pamene adam’bweretsera akavalo oyera otulidwa bwino kwambiri madzulo ena. Adati: “Ndithu, ine ndakonda chuma Chadziko lapansi kuposa Kukumbukira Mbuye wanga mpaka Lidabisala (kulowa) kuseri kwa Chotsekereza. Ndibwezereni kwa ine.” (Surah Saad, aya 31-33). ZOCHITIKA ZOKHUDZA ZA Mahatchi 1. Mahatchi akhala akugwiritsidwa ntchito ndi anthu kukwera ndi, …
Read More »
Ummati Islamic Website













